2 Kings 4:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana uja atakula, tsiku lina adapita kwa bambo wake amene ankayang'anira anthu odula tirigu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atakula mwanayo, linadza tsiku lakuti anatuluka kunka kwa atate wake, ali kwa omweta tirigu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana uja anakula, ndipo tsiku lina anapita kwa abambo ake amene anali ndi anthu odula tirigu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atakula mwanayo, linadza tsiku lakuti anaturuka kumka kwa atate wace, ali kwa omweta tirigu.