2 Kings 4:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwadzidzidzi mwanayo adalira mofuula kwa bambo wake kuti, “Mayo! Mutu wanga ine! Mutu wanga ine!” Bambo wake uja adauza wantchito wake kuti, “Kampereke kwa mai wake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati kwa atate wake, Mutu wanga, mutu wanga! Pamenepo anati kwa mnyamata, Umnyamule umuke naye kwa amake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwanayo anafuwula kwa abambo ake kuti, “Mayo! Mutu wanga ine! Mayo! Mutu wanga ine!” Abambo akewo anawuza wantchito wake kuti, “Munyamule ndi kukamupereka kwa amayi ake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natikwa atate wace, Mutu wanga, mutu wanga! Pamenepo anati kwa mnyamata, Umnyamule umuke naye kwa amace.