2 Kings 4:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thamanga msanga ukamchingamire, ndipo ukamufunse kuti, ‘Kodi nkwabwino? Kodi mwamuna wanu ali bwino? Nanga mwana uja ali bwino?’ ” Mkaziyo adayankha Gehazi kuti, “Inde, nkwabwino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
uthamange tsopano kukomana naye, nunene naye, Muli bwino kodi? Mwamuna wanu ali bwino? Mwanayo ali bwino? Ndipo anati, Ali bwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Thamanga msanga ukakumane naye ndipo ukamufunse kuti, ‘Kodi muli bwino? Kodi mwamuna wanu ali bwino? Kodi mwana wanu ali bwino?’ ” Mayiyo anayankha kuti, “Zonse zili bwino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
uthamange tsopano kukomana naye, nunene naye, Muli bwino kodi? mwamuna wanu ali bwino? mwanayo ali bwino? Ndipo anati, Ali bwino.