2 Kings 4:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mkaziyo adati, “Kodi inu mbuyanga, ine ndidaakupemphani mwana? Kodi suja ndidaakuuzani kuti musandinamize?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkaziyo anati, Ngati ndinapempha mwana kwa mbuyanga? Kodi sindinati, Musandinyenga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mayiyo anati, “Mbuye wanga, kodi ine ndinakupemphani mwana? Kodi sindinakuwuzeni kuti musandinamize?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkaziyo anati, Ngati ndinapempha mwana kwa mbuyanga? Kodi sindinati, Musandinyenga?