2 Kings 4:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mai wake wa mwana uja adati, “Pali Chauta wamoyo, ndiponso pali inu nomwe, ine ndiye sindikusiyani ai.” Tsono Elisa adanyamuka natsatira maiyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma make wa mwana anati, Pali Yehova, pali inunso, ngati nkukusiyani. Ndipo ananyamuka, namtsata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mayi wake wa mwana uja anati, “Pali Yehova wamoyo ndiponso pali inu nomwe, ineyo sindidzakusiyani.” Choncho Elisa ananyamuka natsatira mayiyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mace wa mwana anati, Pali Yehova, pali inunso, ngati nkukusiyani. Ndipo ananyamuka, namtsata.