2 Kings 4:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Elisa ataloŵa m'chipinda muja adaona mwana wakufayo atamgoneka pabedi pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Elisa analowa m'nyumba, taonani, mwanayo ngwakufa, adamgoneka pakama pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Elisa atafika ku nyumbako, taonani, mwanayo anali wakufa atamugoneka pa bedi lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Elisa analowa m'nyumba, taonani, mwanayo ngwakufa, adamgoneka pakama pace.