2 Kings 4:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo maiyo adagwada pa mapazi a Elisa, naŵeramitsa mutu wake pansi. Kenaka adanyamula mwana wake uja, natuluka pa bwalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye nalowa, nagwa pa mapazi ake, nadziweramitsa pansi; nanyamula mwana wake, natuluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayiyo analowa, nagwada pa mapazi a Elisa, naweramitsa mutu wake pansi. Kenaka ananyamula mwana wake natuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye nalowa, nagwa pa mapazi ace, nadziweramitsa pansi; nanyamula mwana wace, naturuka.