2 Kings 4:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero wantchitoyo adaŵagaŵira anthuwo chakudyacho, naadya, ndipo adasiyako, monga momwe Chauta adaanenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero anawagawira, nadya, nasiyapo, monga mwa mau a Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono iye anachipereka kwa anthuwo ndipo anadya china nʼkutsalako, molingana ndi mawu a Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero anawagawira, nadya, nasiyapo, monga mwa mau a Yehova.