2 Kings 4:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono maiyo adauza mwamuna wake kuti, “Tsopano ndikudziŵa kuti munthu amene amadutsa pano kaŵirikaŵiriyu ngwoyera wa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkaziyo anati kwa mwamuna wake, Taona, tsopano ndidziwa kuti munthu uyu wakupitira pathu pano chipitire ndiye munthu woyera wa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayiyo anawuza mwamuna wake kuti, “Taonani, ine ndikudziwa kuti munthu amene amadutsa pano nthawi zambiriyu ndi munthu woyera wa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkaziyo anati kwa mwamuna wace, Taona, tsopano ndidziwa kuti munthu uyu wakupitira pathu pano cipitire ndiye munthu woyera wa Mulungu.