2 Kings 5:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Elisa adamtumira wamthenga kukamuuza kuti, “Pitani mukasambe mu mtsinje wa Yordani kasanunkaŵiri, ndipo muchira ndi kuyeretsedwa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Elisa anamtumira mthenga, ndi kuti, Kasambe m'Yordani kasanu ndi kawiri, ndi mnofu wako udzabwerera momwe, nudzakhala wokonzeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Elisa anatumiza uthenga kwa iye woti, “Pita, kasambe kasanu ndi kawiri mu mtsinje wa Yorodani, thupi lako lidzachira ndi kukhalanso monga kale ndipo udzayeretsedwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Elisa anamtumira mthenga, ndi kuti, Kasambe m'Yordano kasanu ndi kawiri, ndi mnofu wako udzabwerera momwe, nudzakhala wokonzeka.