2 Kings 5:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi Abana ndi Faripara, mitsinje ya ku Damasiko, siposa mitsinje yonse ya ku Israele kuno? Monga sindikadatha kukasamba m'mitsinje imeneyo ndi kuchiritsidwa?” Pomwepo adapotoloka, nachokapo molunda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanga Abana ndi Faripara, mitsinje ya Damasiko, siiposa kodi madzi onse a m'Israele? Ndilekerenji kukasamba m'mwemo, ndi kukonzeka? Natembenuka, nachoka molunda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Abana ndi Faripara, mitsinje ya ku Damasiko, siyoposa mitsinje ina yonse ya ku Israeli? Kodi sindikanasamba mʼmitsinje imeneyo ndi kuyeretsedwa?” Kotero anatembenuka nachoka ali wokwiya kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanga Abana ndi Faripara, mitsinje ya Damasiko, siiposa kodi madzi onse a m'Israyeli? ndilekerenji kukasamba m'mwemo, ndi kukonzeka? Natembenuka, nacoka morunda.