2 Kings 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mtsikana uja adauza mkazi wa Naamani kuti, “Bwanji kodi osati ambuyanga apite kwa mneneri ku Samariya, kuti mneneriyo akaŵachize khate laoli.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati uyu kwa mbuyake wamkazi, Mbuye wanga akadakhala kwa mneneri ali m'Samariya, akadamchiritsa khate lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsikanayo anawuza mkazi wa Naamani kuti, “Mbuye wanga akanapita kukaonana ndi mneneri amene amakhala ku Samariya, akanachiritsidwa khate lawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati uyu kwa mbuyace wamkazi, Mbuye wanga akadakhala kwa mneneri ali m'Samariya, akadamciritsa khate lace.