2 Kings 5:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naamani atamva zimene adaanena mtsikana uja, adapita kwa mfumu nakaiuza kuti, “Mtsikana amene tidakagwira ku Israele uja wanena kuti ati ndipite ku Samariya, kuti mneneri wakumeneko akandichize.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analowa wina, nauza mbuye wake, kuti, Buthulo lofuma ku dziko la Israele lanena zakutizakuti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Naamani anapita kwa mbuye wake kukamuwuza zomwe mtsikana wochokera ku Israeli ananena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analowa wina, nauza mbuye wace, kuti, Buthulo lofuma ku dziko la Israyeli lanena zakuti zakuti.