2 Kings 6:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina ena a m'gulu la aneneri adauza Elisa kuti, “Onani, malo tikukhala ndi inu ano akutichepera kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a aneneri anati kwa Elisa, Taonani tsono, pamalo tikhalapo ife pamaso panu patichepera
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a aneneri anati kwa Elisa, “Taonani malo amene timakhala ndi inu atichepera kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a aneneri anati kwa Elisa, Taonani tsono, pamalo tikhalapo ife pamaso panu paticepera