2 Kings 6:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumuyo idati, “Pitani mukaone kumene akukhala, kuti nditumeko anthu, akamgwire.” Anthuwo atabwerako, adamuuza kuti, “Ali ku Dotani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iye, Kamuoneni komwe ali; ndikatume munthu kumtenga. Ndipo anamuuza kuti, Ali ku Dotani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho mfumu inalamula kuti, “Pitani, kafufuzeni kumene akukhala kuti ine nditume anthu kukamugwira.” Anthuwo anabweretsa mawu oti, “Taonani, Elisa ali ku Dotani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iye, Kamuoneni komwe ali; ndikatume munthu kumtenga. Ndipo anamuuza kuti, Ali ku Dotana.