2 Kings 6:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Elisa adauza ankhondowo kuti, “Njira si imeneyi, ndipo mzinda si umenewunso ai. Tsatani ine, ndikakufikitsani kwa munthu amene mukumfunafunayo.” Choncho adaŵatsogolera mpaka ku Samariya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Elisa ananena nao, Ngati njira ndi iyi? Ngati mudzi ndi uwu? Munditsate ine, ndidzakufikitsani kwa munthu mumfunayo; nawatsogolera ku Samariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Elisa anawawuza ankhondowo kuti, “Njira si imeneyi ndipo mzinda sumenewunso. Tsateni, ndipo ndidzakutengerani kwa munthu amene mukumufunayo.” Ndipo anawatengera ku Samariya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Elisa ananena nao, Ngati njira ndi iyi? ngati mudzi ndi uwu? munditsate ine, ndidzakufikitsani kwa munthu mumfunayo; nawatsogolera ku Samariya.