2 Kings 6:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu ya ku Israele itaona ankhondowo, idafunsa Elisa kuti, “Bambo wanga, kodi ndiŵaphe? Kodi ndiŵaphe?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Niti mfumu ya Israele kwa Elisa pakuwaona, Atate wanga, ndiwakanthe kodi, ndiwakanthe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu ya ku Israeli itawaona, inafunsa Elisa kuti, “Abambo anga, kodi ndiwaphe? Kodi ndiwaphe?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Niti mfumu ya Israyeli kwa Elisa pakuwaona, Atate wanga ndiwakanthe kodi, ndiwakanthe?