2 Kings 6:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Elisa adayankha kuti, “Usaŵaphe ai. Kodi ungaŵaphe anthu amene udachita kuŵagwira ukapolo pomenyana nawo nkhondo? Iyai, koma apatseni chakudya ndi madzi kuti ayambe apeza bwino, kenaka apite kwa mbuyao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati, Musawakanthe; kodi mumakantha omwe mwawagwira ndi lupanga ndi uta wanu? Apatseni mkate ndi madzi adye namwe, namuke kwa mbuye wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Elisa anayankha kuti, “Musawaphe. Kodi mungaphe anthu amene munawagwira pogwiritsa ntchito lupanga ndi uta? Apatseni chakudya ndi madzi kuti adye ndi kumwa kenaka apite kwa mbuye wawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati, Musawakanthe; kodi mumakantha omwe mwawagwira ndi lupanga ndi uta wanu? apatseni mkate ndi madzi adye namwe, namuke kwa mbuye wao.