2 Kings 6:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita nthaŵi ndithu, Benihadadi mfumu ya ku Siriya, adasonkhanitsa gulu lake lankhondo, napita kukazinga Samariya ndi zithando zankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zitatha izi, Benihadadi mfumu ya Aramu anamemeza khamu lake lonse, nakwera, namangira misasa Samariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita nthawi, Beni-Hadadi mfumu ya Aramu anasonkhanitsa gulu lake lonse la ankhondo, napita kukazungulira mzinda wa Samariya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zitatha izi, Benihadadi mfumu ya Aramu anamemeza khamu lace lonse, nakwera, namangira misasa Samariya.