2 Kings 6:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina mfumu ikuyenda pa makoma a mzinda, mai wina adamfuulira kuti, “Inu mbuyanga mfumu, thandizeni.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo popita mfumu ya Israele alikuyenda palinga, mkazi anamfuulira, nati, Ndithandizeni, mbuye wanga mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene mfumu inkayenda pa khoma la mzindawo, mayi wina anafuwulira mfumuyo kuti, “Thandizeni mbuye wanga mfumu!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo popita mfumu ya Israyeli alikuyenda palinga, mkazi anampfuulira, nati, Ndithandizeni, mbuye wanga mfumu.