2 Kings 6:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga chakuvuta nchiyani?” Iyeyo adayankha kuti, “Tsiku lina mai uyu adandiwuza kuti, ‘Ipha mwana wako kuti tidye lero, wanga tidye maŵa.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanena naye mfumu, Ufunanji? Nati iye, Mnzanga uyu ananena ndi ine, Tenga mwana wako timudye lero, ndi mwana wanga timudye mawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mfumuyo inafunsa mayiyo kuti, “Kodi chakuvuta nʼchiyani?” Iye anayankha kuti, “Mayi uyu anandiwuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako kuti timudye lero, ndipo mawa tidzadya mwana wangayu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanena naye mfumu, Ufunanji? Nati iye, Mnzanga uyu ananena ndi ine, Tenga mwana wako timudye lero, ndi mwana wanga timudye mawa.