2 Kings 6:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero tidaphika mwana wangayo, ndipo tidadya. Tsono m'maŵa mwake ndidamuuza kuti, ‘Iphatu mwana wako uja kuti tidye.’ Koma iyeyu wabisa mwana wakeyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tinaphika mwana wanga ndi kumudya, ndi mawa wake ndinanena naye, Tenga mwana wako, timudye; koma wambisa mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho tinaphika mwana wanga ndi kumudya. Tsiku lotsatira lakelo ine ndinati, ‘Bweretsa mwana wako kuti timudye,’ koma iye anabisa mwana wakeyo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tinaphika mwana wanga ndi kumudya, ndi mawa wace ndinanena naye, Tenga mwana wako, timudye; koma wambisa mwana wace.