2 Kings 6:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu ija idati, “Mulungu andiphe, ndikapanda kudulitsa mutu wa Elisa mwana wa Safati lero.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iye, Andilange Mulungu naonjezeko, ngati mutu wa Elisa mwana wa Safati uti ukhale pa iye lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumuyo inati, “Mulungu andilange, andilange kwambiri ndikapanda kudula mutu wa Elisa mwana wa Safati lero!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iye, Andilange Mulungu naonjezeko, ngati mutu wa Elisa mwana wa Safati uti ukhale pa iye lero lino.