2 Kings 6:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Elisayo adapita nawo. Atafika ku Yordani, anthu aja adayamba kudula mitengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namuka nao, nafika ku Yordani, iwo natema mitengo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anapita nawo. Anapita ku Yorodani nayamba kudula mitengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namuka nao, nafika ku Yordano, iwo natema mitengo.