2 Kings 6:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi ina mfumu ya ku Siriya inkamenyana nkhondo ndi Aisraele. Ndipo idapangana ndi aphungu ake kuti, “Tikamange zithando zathu pa malo akutiakuti.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu ya Aramu inalinkuchita nkhondo ndi Israele, nipangana ndi anyamata ake, kuti, Misasa yanga idzakhala pakutipakuti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mfumu ya ku Aramu inali pa nkhondo ndi Israeli. Itakambirana ndi atsogoleri ake ankhondo inati, “Ndidzamanga misasa yanga pamalo akutiakuti.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu ya Aramu inalinkucita nkhondo ndi Israyeli, nipangana ndi anyamata ace, kuti, Misasa yanga idzakhala pakuti pakuti.