2 Kings 8:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Elisa adayankha kuti, “Chauta wandiwonetsa kuti adzafa, komabe pita ukamuuze kuti adzachira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanena naye Elisa, Kamuuze, kuti, Sudzachira konse; popeza Yehova wandionetsa kuti adzafa ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Elisa anayankha kuti, “Pita ndipo ukamuwuze kuti, ‘Udzachira ndithu,’ koma Yehova wandionetsa kuti adzafabe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanena naye Elisa, Kamuuze, kuti, Sudzacira konse; popeza Yehova wandionetsa kuti adzafa ndithu.