2 Kings 8:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atatero, Elisa adamuyang'ana kwambiri Hazaele mpaka adachita manyazi. Apo Elisayo adayamba kulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamyang'ana chidwi, mpaka anachita manyazi, nalira misozi munthu wa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Elisa anamuyangʼana kwambiri Hazaeli mpaka anachita manyazi. Pamenepo munthu wa Mulungu anayamba kulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamyang'ana cidwi, mpaka anacita manyazi, nalira misozi munthu wa Mulungu.