2 Kings 8:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka chachisanu cha ufumu wa Yoramu, mwana wa Ahabu mfumu ya ku Israele, Yehoramu, mwana wa Yehosafati mfumu ya ku Yuda, adayambapo kulamulira dziko la Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chaka chachisanu cha Yoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Israele, pokhala Yehosafati mfumu ya Yuda, Yehoramu mwana wa Yehosafati analowa ufumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chaka chachisanu cha ufumu wa Yoramu mwana wa Ahabu mfumu ya ku Israeli, Yehosafati ali mfumu ya ku Yuda, Yehoramu mwana wake anakhala mfumu ya Ayuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo caka cacisanu ca Yoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Israyeli, pokhala Yehosafati mfumu ya Yuda, Yehoramu mwana wa Yehosafati analowa ufumu.