2 Kings 8:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi yakeyo anthu a ku Edomu adaukira ulamuliro wa Yuda ndipo adadzisankhira mfumu yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku ake Aedomu anapanduka ku ulamuliro wa Yuda, nadziikira mfumu okha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi ya Yehoramu, Edomu anawukira ulamuliro wa Yuda ndipo anadzisankhira mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku ace Aedomu anapanduka ku ulamuliro wa Yuda, nadziikira mfumu okha.