2 Kings 8:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka cha 12 cha ufumu wa Yoramu, mwana wa Ahabu, mfumu ya ku Israele, Ahaziya mwana wa Yehoramu, mfumu ya ku Yuda, adayamba kulamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chakhumi ndi ziwiri cha Yoramu mwana wa Ahabu mfumu Ahaziya mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha khumi ndi chiwiri cha Yoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Israeli, Ahaziya mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda anayamba kulamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cakhumi ndi ziwiri ca Yoramu mwana wa Ahabu mfumu Ahaziya mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda analowa ufumu wace.