2 Kings 8:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono zitatha zaka zisanu ndi ziŵirizo, mai uja adabwerako ku dziko la Afilisti kuja, ndipo adapitanso kwa mfumu ya ku Israele kukafunsa za nyumba yake ndi munda wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakutha pake pa zaka zisanu ndi ziwirizo, mkaziyo anabwera kuchoka m'dziko la Afilisti, natuluka kukanena za nyumba yake ndi munda wake kwa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zitatha zaka zisanu ndi ziwirizo anabwera kuchokera ku dziko la Afilisti ndipo anapita kwa mfumu kukafunsa za nyumba yake ndi munda wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakutha pace pa zaka zisanu ndi ziwirizo, mkaziyo anabwera kucoka m'dziko la Afilisti, naturuka kukanena za nyumba yace ndi munda wace kwa mfumu.