2 Kings 8:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina Elisa adapita ku Damasiko, pa nthaŵi imene Benihadadi mfumu ya ku Siriya ankadwala. Mfumuyo itamva kuti kwabwera munthu wa Mulungu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Elisa anafika ku Damasiko, podwala Benihadadi mfumu ya Aramu; ndipo anamuuza, kuti, Munthu wa Mulungu wadza kuno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Elisa anapita ku Damasiko, ndipo Beni-Hadadi mfumu ya ku Aramu ankadwala. Mfumuyo itawuzidwa kuti, “Munthu wa Mulungu wabwera kuno kuchokera kutali,”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Elisa anafika ku Damasiko, podwala Benihadadi mfumu ya Aramu; ndipo anamuuza, kuti, Munthu wa Mulungu wadza kuno.