2 Kings 9:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iwowo adati, “Iyai ndithu, mutiwuze.” Apo Yehu adati, “Iyeyo wandiwuza mau a Chauta akuti, ‘Ine ndikukudzoza iwe kuti ukhale mfumu ya ku Israele.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iwo, Kunama uku; utifotokozere tsono. Nati iye, Anati kwa ine chakutichakuti; ndi kuti, Atero Yehova, Ndakudzoza mfumu pa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atsogoleri aja anati, “Ukunama! Tiwuze.” Yehu anati, “Zimene wandiwuza ndi izi: ‘Yehova akuti: Ine ndakudzoza iwe kukhala mfumu ya Israeli.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iwo, Kunama uku; utifotokozere tsono. Nati iye, Anati kwa ine cakuti cakuti; ndi kuti, Atero Yehova, Ndakudzoza mfumu pa Israyeli.