2 Kings 9:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukakafika, ukafunefune Yehu, mwana wa Yehosafati, mdzukulu wa Nimisi. Utampeza ukamuuze kuti achokepo pakati pa anzake, ndipo ukaloŵe naye m'chipinda cham'kati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ukafikako, ukaunguzeko Yehu mwana wa Yehosafati mwana wa Nimisi, nulowe numnyamukitse pakati pa abale ake, nupite naye ku chipinda cham'katimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukakafika kumeneko, ukafunefune Yehu mwana wa Yehosafati, mwana wa Nimisi. Ukapite kwa iye, ukamuchotse pakati pa anzake ndi kukamulowetsa mʼchipinda chamʼkati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ukafikako, ukaunguzeko Yehu mwana wa Yehosafati mwana wa Nimsi, nulowe numnyamukitse pakati pa abale ace, nupite naye ku cipinda cam'katimo.