2 Kings 9:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Yoramu adabwevuka nathaŵa, ndipo adafuulira Ahaziya uja kuti, “Iwe Ahaziya, atiwukira anthuŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natembenuza Yoramu manja ake, nathawa, nati kwa Ahaziya, Chiwembu, Ahaziya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoramu anatembenuka, nathawa akufuwula kwa Ahaziya kuti, “Ahaziya, anthuwa atiwukira!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natembenuza Yoramu manja ace, nathawa, nati kwa Ahaziya, Ciwembu, Ahaziya.