2 Kings 9:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yehu adakoka uta ndi mphamvu zake zonse nalasa Yoramu kumsana pakati pa mapewa, kotero kuti muvi udaloŵa mpaka ku mtima, ndipo adagwera m'galeta momwemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nafa nao Yehu uta wake, nalasa Yoramu pachikota, nutuluka muvi pa mtima wake, naonyezeka iye m'galeta wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Yehu anakoka uta wake ndipo analasa Yoramu kumsana pakati pa mapewa. Muviwo unakalasa mtima wake ndipo anagwa pansi mʼgaleta lakelo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nafa nao Yehu uta wace, nalasa Yoramu pacikota, nuturuka mubvi pa mtima wace, naonyezeka iye m'gareta wace.