2 Kings 9:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nduna zake zidamnyamulira m'galeta kunka naye ku Yerusalemu, ndipo zidamuika m'manda momwe adaikidwa makolo ake mu mzinda wa Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anyamata ake anamnyamulira pagaleta kunka naye ku Yerusalemu, namuika ku manda ake pamodzi ndi makolo ake m'mudzi wa Davide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Antchito ake anamunyamulira mʼgaleta kupita naye ku Yerusalemu ndipo anamuyika mʼmanda pamodzi ndi makolo ake mu mzinda wa Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anyamata ace anamnyamulira pagareta kumka naye ku Yerusalemu, namuika ku manda ace pamodzi ndi makolo ace m'mudzi wa Davide.