2 Kings 9:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka cha 11 cha ufumu wa Yoramu mwana wa Ahabu, mpamene Ahaziya adaayamba kulamulira Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pa chaka chakhumi ndi chimodzi cha Yoramu mwana wa Ahabu, Ahaziya analowa ufumu pa Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Mʼchaka cha khumi ndi chimodzi cha ufumu wa Yoramu mwana wa Ahabu, Ahaziya anakhala mfumu ya ku Yuda).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pa caka cakhumi ndi cimodzi ca Yoramu mwana wa Ahabu, Ahaziya analowa ufumu pa Yuda.