2 Kings 9:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ukathire mafutaŵa pamutu pake, ndipo ukanene kuti, ‘Chauta akukudzoza kuti ukhale mfumu ya ku Israele.’ Pomwepo ukatsekule chitseko ndipo ukathaŵe, usakachedwe ai.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nutenge nsupa ya mafutayo, nuwatsanulire pamutu pake, nunene, Atero Yehova, Ndakudzoza iwe ukhale mfumu pa Israele. Utatero, tsegula pakhomo, nuthawe osachedwa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ukatenge botololi ndi kuthira mafuta pa mutu wake ndipo ukanene kuti, ‘Yehova akuti, Ine ndikudzoza iwe kukhala mfumu ya Israeli.’ Kenaka ukatsekule chitseko ndi kuthawa ndipo usakachedwe!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nutenge nsupa ya mafutayo, nuwatsanulire pamutu pace, nunene, Atero Yehova; Ndakudzoza iwe ukhale mfumu pa Israyeli. Utatero, tsegula pakhomo, nuthawe osacedwa,