2 Kings 9:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pamene Yehu ankaloŵa pa chipata, Yezibeleyo adamkuwira nati, “Inu aZimuri, amene mudapha mbuyanu, kodi ndi zamtendere?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo polowa Yehu pachipata, mkaziyo anati, Mtendere kodi Zimiri, iwe wakupha mbuyako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Yehu ankalowa pa chipata iye anafunsa kuti, “Kodi wabwera mwamtendere, iwe Zimuri, munthu wopha mbuye wako?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo polowa Yehu pacipata, mkaziyo anati, Mtendere kodi Zimri, iwe wakupha mbuyako?