2 Kings 9:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yehu adayang'ana ku zenera nati, “Kodi akugwirizana ndi ine ndani?” Tsono atumiki aŵiri kapena atatu a ku bwalo la mfumu adayang'ana Yehu uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anakweza maso ake kuzenera, nati, Ali ndi ine ndani? Ndani? Nampenyererako adindo awiri kapena atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehu anakweza maso nayangʼana pa zenera, ndipo anafuwula kuti, “Kodi ndani ali mbali yanga? Ndani?” Anthu ofulidwa awiri kapena atatu anayangʼana Yehu pansipo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anakweza maso ace kuzenera, nati, Ali ndi ine ndani? Ndani? Nampenyererako adindo awiri kapena atatu.