2 Kings 9:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo adaŵalamula kuti, “Mponyeni pansi mkaziyo.” Pomwepo iwo adamponya pansi, ndipo magazi ake ena adafalikira pa khoma ndi pa akavalo. Kenaka Yehu adayendetsa akavalo ake nkumpondereza mkaziyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iye, Mgwetsereni pansi. Namgwetsera pansi, nuwazikako mwazi wake pakhoma ndi pa akavalo, nampondereza iye pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehu anawawuza kuti, “Muponyeni pansi!” Motero anamuponya pansi ndipo magazi ake ena anafalikira pa khoma ndi pa akavalo pamene ankamupondaponda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iye, Mgwetsereni pansi. Namgwetsera pansi, nuwazikako mwazi wace pakhoma ndi pa akavalo, nampondereza iye pansi.