2 Kings 9:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yehu adaloŵa m'nyumba yaufumu naadya ndi kumwa. Kenaka adati, “Kamtoleni mkazi wotembereredwa uja, mukamuike, pakuti ndi mwana wa mfumu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atalowa, anadya namwa, nati, Kampenyeni tsono mkazi wotembereredwa uyu, nimumuike; popeza ndiye mwana wa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehu analowa mʼnyumba yaufumu ndipo anadya ndi kumwa. Kenaka iye anati, “Kamutoleni mkazi wotembereredwayo, ndipo kamuyikeni mʼmanda, popeza ndi mwana wa mfumu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atalowa, anadya namwa, nati, Kampenyeni tsono mkazi wotembereredwa uyu, nimumuike; popeza ndiye mwana wa mfumu.