2 Kings 9:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamene ankapita kuti akamuike, sadapezepo nkanthu komwe koma chibade, mapazi ndi zikhatho za manja ake basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namuka iwo kuti amuike; koma sanapezeko kanthu kena koma bade, ndi mapazi, ndi zikhato za manja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma atapita kuti akamuyike mʼmanda, sanapeze kanthu kupatula chibade cha mutu wokha, mapazi ake ndi manja ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namuka iwo kuti amuike; koma sanapezako kanthu kena koma bade, ndi mapazi, ndi zikhato za manja.