2 Kings 9:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mtembo wakewo udzakhala ngati ndoŵe pa munda m'dziko la Yezireele, kotero kuti palibe ndi mmodzi yemwe amene adzatha kunena kuti, “Uyu ndi Yezibele.” ’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi thupi la Yezebele lidzakhala ngati ndowe pamunda m'dera la Yezireele, kuti sadzati, Ndi Yezebele uyu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtembo wa Yezebeli udzakhala ngati zinyalala pa munda wa ku Yezireeli, kotero kuti palibe amene adzathe kunena kuti, ‘Uyu ndi Yezebeli.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi thupi la Yezebeli lidzakhala ngati ndowe pamunda m'dera la Yezreeli, kuti sadzati, Ndi Yezebeli uyu.