2 Kings 9:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu banja lonse la Ahabu lidzatha phu! Ku Israele adzapha mwamuna aliyense wa banja la Ahabu, kapolo kapena mfulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza nyumba yonse ya Ahabu idzaonongeka, ndipo ndidzalikhira Ahabu ana amuna onse womangika ndi womasuka m'Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Banja lonse la Ahabu lidzatheratu. Ndidzachotsa munthu aliyense wamwamuna wa banja la Ahabu kaya ndi kapolo kapena mfulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza nyumba yonse ya Ahabu idzaonongeka, ndipo ndidzalikhira Ahabu ana amuna onse womangika ndi womasuka m'Israyeli.