2 Peter 1:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma choyamba mumvetse kuti munthu payekha sangathe kumasulira mau a aneneri olembedwa m'Malembo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kudziwa ichi poyamba, kuti palibe chinenero cha lembo chitanthauzidwa pa chokha,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuposa zonse, inu muyenera kuzindikira kuti palibe mawu a uneneri amene amatanthauzidwa pa okha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kudziwa ici poyamba, kuti palibe cinenero ca lembo citanthauzidwa pa cokha,