2 Peter 2:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adasiya njira yolungama, adasokera potsata njira ya Balamu, mwana wa Beori, amene ankafunitsa kupata mphotho pochita zosalungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
posiya njira yolunjika, anasokera, atatsata njira ya Balamu mwana wa Beori, amene anakonda mphotho ya chosalungama;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anasiya njira yolungama ndipo anapatuka kutsata njira ya Baalamu mwana wa Beori, amene anakonda malipiro a chosalungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
posiya njira yolunjika, anasokera, atatsata njira ya Balamu mwana wa Beori, amene anakonda mphotho ya cosalungama;