2 Peter 2:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma adapulumutsa Loti munthu wolungama, amene ankavutika ndi makhalidwe odzilekerera a anthu ochimwa aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anapulumutsa Loti wolungamayo, wolema mtima ndi mayendedwe onyansa a oipa aja
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Iye anapulumutsa Loti, munthu wolungama, amene ankavutika ndi khalidwe lonyansa la anthu oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anapulumutsa Loti wolungamayo, wolema mtima ndi mayendedwe onyansa a oipa aja