2 Samuel 1:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Davide adafunsa mnyamata wodzanena uja kuti, “Kodi iwe ndiwe wa kuti?” Iye adati, “Munthune ndine mwana wa mlendo, Mwamaleke.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide ananena ndi mnyamata wakumuuzayo, Kwanu nkuti? Nayankha, Ine ndine mwana wa mlendo, Mwamaleke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anati kwa mnyamata amene anabweretsa uthengawo, “Iwe umachokera kuti?” Iye anayankha kuti, “Ine ndine mwana wa mlendo Mwamaleki.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide ananena ndi mnyamata wakumuuzayo, Kwanu nkuti? Nayankha, Ine ndine mwana wa mlendo, M-amaleki.